1 Mafumu 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwalo lalikulu linazunguliridwa ndi khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu kuchokera pansi ndi mzere umodzi wa matabwa a mkungudza pamwamba pake. Ndi mmenenso zinalili ndi bwalo lamkati+ la nyumba ya Yehova komanso khonde la nyumbayo.+
12 Bwalo lalikulu linazunguliridwa ndi khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu kuchokera pansi ndi mzere umodzi wa matabwa a mkungudza pamwamba pake. Ndi mmenenso zinalili ndi bwalo lamkati+ la nyumba ya Yehova komanso khonde la nyumbayo.+