1 Mbiri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Magulu a mbadwa za ana a Aroni anali awa: Ana a Aroni anali Nadabu, Abihu,+ Eliezara ndi Itamara.+ 1 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Magulu a alonda apageti+ anali awa: Pa mbadwa za Kora panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.
24 Magulu a mbadwa za ana a Aroni anali awa: Ana a Aroni anali Nadabu, Abihu,+ Eliezara ndi Itamara.+
26 Magulu a alonda apageti+ anali awa: Pa mbadwa za Kora panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.