-
1 Mbiri 23:30, 31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Mʼmawa uliwonse ankaimirira+ kuti athokoze ndi kutamanda Yehova. Madzulo ankachitanso zimenezi.+ 31 Ankathandizanso pa nthawi iliyonse yopereka nsembe zopsereza kwa Yehova pa Masabata,+ pa masiku amene mwezi watsopano waoneka+ ndi pa nthawi ya zikondwerero.+ Ankachita zimenezi nthawi zonse pamaso pa Yehova, malinga ndi ziwerengero zake zogwirizana ndi malamulo ake.
-