2 Mbiri 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya zamʼnyumba ya Mulungu woona+ nʼkuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko za nyumba ya Yehova.+ Kenako anadzimangira maguwa ansembe mʼmakona onse a mu Yerusalemu.
24 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya zamʼnyumba ya Mulungu woona+ nʼkuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko za nyumba ya Yehova.+ Kenako anadzimangira maguwa ansembe mʼmakona onse a mu Yerusalemu.