Maliko 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno anakhala pansi pamalo amene ankatha kuona moponyeramo zopereka*+ ndipo anayamba kuona mmene gulu la anthu linkaponyera ndalama moponyera zoperekamo. Anaona anthu ambiri olemera akuponyamo makobidi ambiri.+
41 Ndiyeno anakhala pansi pamalo amene ankatha kuona moponyeramo zopereka*+ ndipo anayamba kuona mmene gulu la anthu linkaponyera ndalama moponyera zoperekamo. Anaona anthu ambiri olemera akuponyamo makobidi ambiri.+