-
2 Mafumu 12:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako wansembe Yehoyada anatenga bokosi+ nʼkuboola kachibowo pachivundikiro chake. Kenako anaika bokosilo pambali pa guwa lansembe mbali yakumanja, munthu akamalowa mʼnyumba ya Yehova. Ansembe omwe ankalondera pakhomo ankaika mʼbokosilo ndalama zonse zimene anthu ankabweretsa kunyumba ya Yehova.+
-