2 Mafumu 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akaona kuti mʼbokosilo muli ndalama zambiri, mlembi wa mfumu ndi mkulu wa ansembe ankabwera nʼkuwerenga komanso kuika* mʼtimatumba ndalama zimene zinkaperekedwa panyumba ya Yehova.+
10 Akaona kuti mʼbokosilo muli ndalama zambiri, mlembi wa mfumu ndi mkulu wa ansembe ankabwera nʼkuwerenga komanso kuika* mʼtimatumba ndalama zimene zinkaperekedwa panyumba ya Yehova.+