Ekisodo 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero anapanga ziwiya zapatebulolo, mbale zake, makapu, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Anazipanga ndi golide woyenga bwino.+ Numeri 7:84 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Potsegulira guwa lansembe, pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri a Isiraeli anapereka izi:+ Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva 12 ndi makapu agolide 12.+
16 Atatero anapanga ziwiya zapatebulolo, mbale zake, makapu, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Anazipanga ndi golide woyenga bwino.+
84 Potsegulira guwa lansembe, pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri a Isiraeli anapereka izi:+ Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva 12 ndi makapu agolide 12.+