2 Mafumu 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa nthawi imeneyo Hazaeli+ mfumu ya Siriya anapita kukamenyana ndi anthu amumzinda wa Gati+ nʼkuulanda. Kenako Hazaeli anaganiza zokaukira Yerusalemu.+
17 Pa nthawi imeneyo Hazaeli+ mfumu ya Siriya anapita kukamenyana ndi anthu amumzinda wa Gati+ nʼkuulanda. Kenako Hazaeli anaganiza zokaukira Yerusalemu.+