-
2 Mbiri 24:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Yehoyada atamwalira, akalonga a Yuda anabwera nʼkudzagwada pamaso pa mfumu ndipo mfumuyo inawamvera. 18 Iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo nʼkuyamba kutumikira mizati yopatulika* ndiponso mafano. Choncho Mulungu anakwiyira kwambiri Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kulakwa kwawoko.
-