2 Mbiri 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa makolo athu akhala akuchita zosakhulupirika ndiponso zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya komanso anasiya chihema chopatulika cha Yehova nʼkumulozetsa nkhongo.+ Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+
6 Chifukwa makolo athu akhala akuchita zosakhulupirika ndiponso zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya komanso anasiya chihema chopatulika cha Yehova nʼkumulozetsa nkhongo.+
6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+