1 Mbiri 9:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alonda apageti+ anali Salumu, Akubu, Talimoni ndi Ahimani ndipo mʼbale wawo Salumu ndi amene anali mtsogoleri. 18 Mpaka nthawi imeneyo, iye ankakhala pageti la mfumu la mbali yakumʼmawa.+ Amenewa anali alonda a pamageti a misasa ya Alevi.
17 Alonda apageti+ anali Salumu, Akubu, Talimoni ndi Ahimani ndipo mʼbale wawo Salumu ndi amene anali mtsogoleri. 18 Mpaka nthawi imeneyo, iye ankakhala pageti la mfumu la mbali yakumʼmawa.+ Amenewa anali alonda a pamageti a misasa ya Alevi.