Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 27:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Amenewa ndi malamulo amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa Aisiraeli.

  • Numeri 36:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Amenewa ndi malamulo ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa Aisiraeli kudzera mwa Mose ku Yeriko, mʼchipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+

  • Deuteronomo 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Awa ndi malangizo ndi zigamulo zimene muyenera kutsatira mosamala, masiku onse amene mudzakhale mʼdziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu adzakupatseni kuti likhale lanu.

  • Nehemiya 9:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Mafumu athu, akalonga athu, ansembe athu ndi makolo athu sanatsatire Chilamulo chanu ndipo sanamvere malamulo anu kapena zikumbutso zanu zowachenjeza.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena