Nehemiya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthawi yonseyi ine sindinali ku Yerusalemu, chifukwa mʼchaka cha 32+ cha ulamuliro wa Aritasasita+ mfumu ya Babulo, ndinabwerera kwa mfumu. Ndiyeno patapita nthawi, ndinapempha mfumuyo kuti ndichoke kwakanthawi.
6 Nthawi yonseyi ine sindinali ku Yerusalemu, chifukwa mʼchaka cha 32+ cha ulamuliro wa Aritasasita+ mfumu ya Babulo, ndinabwerera kwa mfumu. Ndiyeno patapita nthawi, ndinapempha mfumuyo kuti ndichoke kwakanthawi.