Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma pamene ndinasowa zofunika zina ndili kwanuko, sindinalemetse munthu aliyense, popeza abale amene anachokera ku Makedoniya anandipatsa zonse zimene ndinkafunikira.+ Ndithu, ndinayesetsa kuti ndisakulemetseni mʼnjira iliyonse, ndipo ndipitirizabe kutero.+

  • 2 Akorinto 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndine wokonzeka kubwera kwa inu ndipo kano ndi kachitatu kukhala wokonzeka. Koma sindidzakhala katundu wolemetsa chifukwa sindikufuna zinthu zanu,+ koma inuyo. Paja si udindo wa ana+ kusunga chuma kuti chidzathandize makolo awo, koma makolo ndi amene ayenera kusungira chuma ana awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena