Nehemiya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyo Haneni,+ mmodzi wa abale anga, anabwera limodzi ndi amuna ena kuchokera ku Yuda. Ndinawafunsa mmene zinthu zinalili kwa Ayuda amene anathawa ku ukapolo+ komanso za Yerusalemu.
2 Pa nthawiyo Haneni,+ mmodzi wa abale anga, anabwera limodzi ndi amuna ena kuchokera ku Yuda. Ndinawafunsa mmene zinthu zinalili kwa Ayuda amene anathawa ku ukapolo+ komanso za Yerusalemu.