-
Nehemiya 6:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mʼmasiku amenewo, anthu olemekezeka+ a mu Yuda ankalemba makalata ambiri opita kwa Tobia ndipo Tobiayo ankawayankha. 18 Anthu ambiri mu Yuda anamulumbirira kuti akhala kumbali yake chifukwa anali mkamwini wa Sekaniya, mwana wa Ara.+ Ndipo Yehohanani mwana wa Tobia anakwatira mwana wamkazi wa Mesulamu,+ mwana wa Berekiya.
-