Yoswa 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+ Yoswa 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Alimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4. Yeremiya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Awa ndi mawu a Yeremiya* mwana wa Hilikiya, mmodzi wa ansembe a ku Anatoti,+ mʼdera la Benjamini.
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
18 Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Alimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.