Yoswa 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunalinso Gibiyoni,+ Rama, Beeroti, Yoswa 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Chimenechi chinali cholowa cha ana a Benjamini motsatira mabanja awo.
28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Chimenechi chinali cholowa cha ana a Benjamini motsatira mabanja awo.