Yoswa 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Yoswa anatumiza amuna ena kuchokera ku Yeriko kupita ku Ai,+ pafupi ndi Beti-aveni, kumʼmawa kwa Beteli.+ Iye anawauza kuti: “Pitani mukafufuze zokhudza mzindawu.” Amunawo anapita nʼkukafufuza zokhudza mzinda wa Ai.
2 Tsopano Yoswa anatumiza amuna ena kuchokera ku Yeriko kupita ku Ai,+ pafupi ndi Beti-aveni, kumʼmawa kwa Beteli.+ Iye anawauza kuti: “Pitani mukafufuze zokhudza mzindawu.” Amunawo anapita nʼkukafufuza zokhudza mzinda wa Ai.