Ezara 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa ana a Pasuri+ panali Elioenai, Maaseya, Isimaeli, Netaneli, Yozabadi ndi Eleasa. Ezara 10:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Onsewa anatenga akazi achilendo+ ndipo akaziwo ndi ana awo anawatumiza kwawo.+