-
Nehemiya 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Nehemiya, yemwe pa nthawiyo anali bwanamkubwa,* Ezara+ wansembe ndi wokopera Malemba,* komanso Alevi amene ankapereka malangizo kwa anthu, anauza anthuwo kuti: “Lero ndi tsiku lopatulika kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musakhale achisoni ndipo musalire.” Ananena zimenezi chifukwa anthu onse ankalira pamene ankamvetsera mawu a mʼChilamulocho.
-