Levitiko 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Amenewa ndi malamulo amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa Aisiraeli.