-
Nehemiya 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Inu Yehova, chonde mvetserani pemphero la ine mtumiki wanu ndiponso pemphero la atumiki anu amene amaopa dzina lanu ndi mtima wonse. Chonde, ndithandizeni ine mtumiki wanu kuti zinthu zindiyendere bwino lero ndipo munthuyu andichitire chifundo.”+
Pa nthawiyi ndinali woperekera zakumwa kwa mfumu.+
-