Nehemiya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sanibalati+ atangomva kuti tikumanganso mpanda, anakwiya ndiponso anapsa mtima kwambiri moti anapitiriza kunyoza Ayuda. Nehemiya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Bwera tidzapangane nthawi yoti tikakumane mʼmudzi wina mʼchigwa cha Ono.”+ Koma ankandikonzera chiwembu.
4 Sanibalati+ atangomva kuti tikumanganso mpanda, anakwiya ndiponso anapsa mtima kwambiri moti anapitiriza kunyoza Ayuda.
2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Bwera tidzapangane nthawi yoti tikakumane mʼmudzi wina mʼchigwa cha Ono.”+ Koma ankandikonzera chiwembu.