Yohane 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ku Yerusalemu pa Geti la Nkhosa+ pali damu limene mʼChiheberi limatchedwa Betizata. Mʼmbali mwa damulo muli makonde 5 amene ali ndi zipilala.
2 Ku Yerusalemu pa Geti la Nkhosa+ pali damu limene mʼChiheberi limatchedwa Betizata. Mʼmbali mwa damulo muli makonde 5 amene ali ndi zipilala.