Yeremiya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bisalani inu ana a Benjamini, thawani mu Yerusalemu. Imbani lipenga la nyanga+ ya nkhosa ku Tekowa.+Yatsani chizindikiro cha moto ku Beti-hakeremu, Chifukwa tsoka likubwera kuchokera kumpoto ndipo ndi lalikulu kwambiri.+
6 Bisalani inu ana a Benjamini, thawani mu Yerusalemu. Imbani lipenga la nyanga+ ya nkhosa ku Tekowa.+Yatsani chizindikiro cha moto ku Beti-hakeremu, Chifukwa tsoka likubwera kuchokera kumpoto ndipo ndi lalikulu kwambiri.+