Salimo 88:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 88 Inu Yehova, Mulungu amene amandipulumutsa,+Masana ndimafuulira inu,Ndipo usiku ndimabwera pamaso panu.+ Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiye kodi Mulungu sadzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa osankhidwa ake, amene amafuulira kwa iye masana ndi usiku,+ pamene akuwalezera mtima?+
88 Inu Yehova, Mulungu amene amandipulumutsa,+Masana ndimafuulira inu,Ndipo usiku ndimabwera pamaso panu.+
7 Ndiye kodi Mulungu sadzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa osankhidwa ake, amene amafuulira kwa iye masana ndi usiku,+ pamene akuwalezera mtima?+