Nehemiya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atekowa+ anapitiriza kuchokera pamene Zadoki analekezera. Koma anthu otchuka pakati pa Atekowa sanadzichepetse nʼkugwira nawo ntchito ya atsogoleri awo.
5 Atekowa+ anapitiriza kuchokera pamene Zadoki analekezera. Koma anthu otchuka pakati pa Atekowa sanadzichepetse nʼkugwira nawo ntchito ya atsogoleri awo.