Genesis 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iyi ndi mbiri ya Nowa. Nowa anali munthu wolungama.+ Iye anali wopanda cholakwa pakati pa anthu a mʼnthawi yake. Nowa anayenda ndi Mulungu woona.+
9 Iyi ndi mbiri ya Nowa. Nowa anali munthu wolungama.+ Iye anali wopanda cholakwa pakati pa anthu a mʼnthawi yake. Nowa anayenda ndi Mulungu woona.+