Yobu 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amamva phokoso lochititsa mantha mʼmakutu ake,+Pa nthawi yamtendere achifwamba amamuukira. Yobu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inde, kuwala kwa woipa kudzazimitsidwa,Ndipo malawi a moto wake sadzawala.+ Yobu 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zoopsa zimamuchititsa mantha paliponse,+Ndipo zimamuthamangitsa zili naye pafupi kwambiri.