Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa Yehova ndi amene amapereka nzeru.+Kudziwa zinthu komanso kuzindikira zimatuluka mʼkamwa mwake. Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+
6 Chifukwa Yehova ndi amene amapereka nzeru.+Kudziwa zinthu komanso kuzindikira zimatuluka mʼkamwa mwake.
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+