Miyambo 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa nzeru ndi zabwino kwambiri kuposa miyala ya korali.*Zinthu zina zonse zamtengo wapatali sizingafanane nazo. Miyambo 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pali golide komanso miyala yambiri yamtengo wapatali ya korali,*Koma milomo yodziwa zinthu ndi yamtengo wapatali.+
11 Chifukwa nzeru ndi zabwino kwambiri kuposa miyala ya korali.*Zinthu zina zonse zamtengo wapatali sizingafanane nazo.
15 Pali golide komanso miyala yambiri yamtengo wapatali ya korali,*Koma milomo yodziwa zinthu ndi yamtengo wapatali.+