Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Maso a Yehova ali paliponse,

      Amaona anthu oipa ndi abwino omwe.+

  • Zekariya 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munthu asakunyozeni chifukwa chakuti munayamba kumanga ndi zinthu zochepa.+ Popeza anthu adzasangalala ndipo adzaona chingwe choyezera cha mmisiri womanga, mʼdzanja la Zerubabele. Nyale 7 zimenezi* ndi maso a Yehova amene akuyangʼana uku ndi uku padziko lonse lapansi.”+

  • 1 Petulo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena