-
Deuteronomo 32:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Anamudyetsa uchi wochokera mʼthanthwe,
Ndi mafuta ochokera mʼmwala wa nsangalabwi.
-
Anamudyetsa uchi wochokera mʼthanthwe,
Ndi mafuta ochokera mʼmwala wa nsangalabwi.