Miyambo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense amene amatseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,Nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+ Miyambo 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pulumutsa anthu amene atengedwa kuti akaphedwe,Ndipo amene akuyenda modzandira popita kukaphedwa uwathandize.+
13 Aliyense amene amatseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,Nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+
11 Pulumutsa anthu amene atengedwa kuti akaphedwe,Ndipo amene akuyenda modzandira popita kukaphedwa uwathandize.+