-
Deuteronomo 24:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndipo ngati munthuyo ndi wosauka, musamagone ndi chinthu chake chimene wakupatsani kuti chikhale chikolecho.+ 13 Muzionetsetsa kuti mwamubwezera chikolecho dzuwa likangolowa, kuti azipita kukagona ali ndi chofunda chake.+ Mukatero iye adzakudalitsani, ndipo mudzakhala mutachita chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wanu.
-