Luka 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ukakonza phwando, uziitana anthu osauka, otsimphina, olumala ndi osaona.+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+
27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+