Salimo 72:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzakhala ngati mvula imene imagwera pa udzu umene watchetchedwa,Ngati mvula yamvumbi imene imanyowetsa nthaka.+ Miyambo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+
6 Adzakhala ngati mvula imene imagwera pa udzu umene watchetchedwa,Ngati mvula yamvumbi imene imanyowetsa nthaka.+
15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+