Yobu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndakhala chinthu choseketsa kwa anzanga,+Ndakhala munthu amene akuitana Mulungu kuti amuyankhe.+ Munthu wolungama komanso wosalakwa wakhala choseketsa.
4 Ine ndakhala chinthu choseketsa kwa anzanga,+Ndakhala munthu amene akuitana Mulungu kuti amuyankhe.+ Munthu wolungama komanso wosalakwa wakhala choseketsa.