Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova anauza Mose kuti: “Kodi bambo ake akanamulavulira malovu kumaso, sakanakhala wonyozeka kwa masiku 7? Ndiye mʼtulutseni akakhale kunja kwa msasa+ kwa masiku 7, pambuyo pake mumulowetsenso mumsasamo.”

  • Deuteronomo 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 mkazi wamasiyeyo aziyandikira mchimwene wa mwamuna wakeyo akuluwo akuona ndipo azimuvula nsapato+ nʼkumulavulira kumaso nʼkunena kuti, ‘Izi nʼzimene ziyenera kuchitikira munthu amene wakana kumanga nyumba ya mchimwene wake.’

  • Yesaya 50:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Msana wanga ndinaupereka kwa anthu amene ankandimenya

      Ndipo masaya anga ndinawapereka kwa anthu amene ankandizula ndevu.

      Sindinabise nkhope yanga kuti asaichitire zinthu zochititsa manyazi komanso kuti asailavulire.+

  • Mateyu 27:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Atatero anamulavulira+ ndipo anatenga bango lija nʼkuyamba kumumenya nalo mʼmutu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena