Yobu 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mnofu wanga wakutidwa ndi mphutsi komanso fumbi,+Khungu langa langʼambika nʼkumatuluka mafinya.+ Maliro 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala.Anthu sakuthanso kuwazindikira mʼmisewu. Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo wouma.
8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala.Anthu sakuthanso kuwazindikira mʼmisewu. Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo wouma.