Yobu 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu mukudziwa kuti ndine wosalakwa,+Ndipo palibe amene angandipulumutse mʼmanja mwanu.+ Yobu 16:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhope yanga yafiira chifukwa cholira,+Ndipo pazikope zanga pali mdima wandiweyani,*17 Ngakhale kuti manja anga sanachite zachiwawa,Ndipo pemphero langa ndi loyera. Yobu 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mapazi anga akuponda mmene mapazi ake akuponda.Ndapitiriza kuyenda mʼnjira yake ndipo sindinapatuke.+
16 Nkhope yanga yafiira chifukwa cholira,+Ndipo pazikope zanga pali mdima wandiweyani,*17 Ngakhale kuti manja anga sanachite zachiwawa,Ndipo pemphero langa ndi loyera.
11 Mapazi anga akuponda mmene mapazi ake akuponda.Ndapitiriza kuyenda mʼnjira yake ndipo sindinapatuke.+