Yobu 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zikanakhala bwino mukanandibisa mʼManda,*+Mukanandibisa mpaka mkwiyo wanu utadutsa,Zikanakhala bwino mukanandiikira nthawi nʼkudzandikumbukira.+
13 Zikanakhala bwino mukanandibisa mʼManda,*+Mukanandibisa mpaka mkwiyo wanu utadutsa,Zikanakhala bwino mukanandiikira nthawi nʼkudzandikumbukira.+