14 Namani atamva zimenezi, anapita kumtsinje wa Yorodano nʼkukasamba maulendo 7, mogwirizana ndi zimene munthu wa Mulungu woona uja ananena.+ Kenako thupi lake linabwerera mwakale moti khungu lake linakhala ngati la kamnyamata+ ndipo anakhala woyera.+