Salimo 147:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye amapereka sinowo* ngati ubweya wa nkhosa.+Amamwaza mame oundana ngati phulusa.+