Salimo 111:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ntchito za Yehova ndi zazikulu,+ד [Daleth]Anthu onse amene amasangalala nazo amaziphunzira.+ Salimo 145:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo adzanena za mphamvu zanu zodabwitsa+Ndipo ndidzaganizira mozama za ntchito zanu zodabwitsa.