Salimo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa Yehova ndi wolungama.+ Iye amakonda ntchito zolungama.+ Anthu owongoka mtima adzaona nkhope yake.*+ Salimo 71:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Mwachita zinthu zazikulu,Inu Mulungu, ndi ndani angafanane nanu?+
7 Chifukwa Yehova ndi wolungama.+ Iye amakonda ntchito zolungama.+ Anthu owongoka mtima adzaona nkhope yake.*+
19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Mwachita zinthu zazikulu,Inu Mulungu, ndi ndani angafanane nanu?+