Yobu 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munati, ‘Kodi uyu ndi ndani amene akuphimba malangizo anga nʼkumalankhula mopanda nzeruyu?’+ Choncho ndinalankhula, koma mosazindikiraZokhudza zinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+
3 Inu munati, ‘Kodi uyu ndi ndani amene akuphimba malangizo anga nʼkumalankhula mopanda nzeruyu?’+ Choncho ndinalankhula, koma mosazindikiraZokhudza zinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+