Yobu 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa amauza matalala kuti, ‘Gwerani padziko lapansi,’+ Ndipo mvula amaiuza kuti, ‘Igwa mwamphamvu kwambiri.’+
6 Chifukwa amauza matalala kuti, ‘Gwerani padziko lapansi,’+ Ndipo mvula amaiuza kuti, ‘Igwa mwamphamvu kwambiri.’+